2 Mbiri 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ineyo ndipereka chakudya cha antchito anu otola nkhuni ndi odula mitengo. Ndipereka tirigu wokwanira makori* 20,000,+ balere makori 20,000, vinyo mitsuko* 20,000,+ ndi mafuta mitsuko 20,000.”
10 Ineyo ndipereka chakudya cha antchito anu otola nkhuni ndi odula mitengo. Ndipereka tirigu wokwanira makori* 20,000,+ balere makori 20,000, vinyo mitsuko* 20,000,+ ndi mafuta mitsuko 20,000.”