Esitere 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’masiku a Ahasiwero,*+ amene anali kulamulira zigawo 127 monga mfumu, kuchokera ku Indiya mpaka ku Itiyopiya,+ Danieli 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “PERESI,* ufumu wanu wagawanika ndipo waperekedwa kwa Amedi ndi Aperisiya.”+
1 M’masiku a Ahasiwero,*+ amene anali kulamulira zigawo 127 monga mfumu, kuchokera ku Indiya mpaka ku Itiyopiya,+