1 Mafumu 8:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Solomo anapereka nsembe zachiyanjano+ zimene anayenera kupereka kwa Yehova. Anapereka ng’ombe 22,000 ndi nkhosa 120,000+ kuti mfumuyo ndi ana onse a Isiraeli atsegulire+ nyumba ya Yehova.
63 Solomo anapereka nsembe zachiyanjano+ zimene anayenera kupereka kwa Yehova. Anapereka ng’ombe 22,000 ndi nkhosa 120,000+ kuti mfumuyo ndi ana onse a Isiraeli atsegulire+ nyumba ya Yehova.