Ekisodo 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Taona, ndakuika kuti ukhale Mulungu kwa Farao,+ ndipo Aroni m’bale wako akhala mneneri wako.+ Ekisodo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Koma iwe patula Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake pakati pa ana a Isiraeli, ndipo Aroniyo+ atumikire monga wansembe wanga pamodzi ndi ana akewo,+ Nadabu, Abihu,+ Eleazara ndi Itamara.+
7 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Taona, ndakuika kuti ukhale Mulungu kwa Farao,+ ndipo Aroni m’bale wako akhala mneneri wako.+
28 “Koma iwe patula Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake pakati pa ana a Isiraeli, ndipo Aroniyo+ atumikire monga wansembe wanga pamodzi ndi ana akewo,+ Nadabu, Abihu,+ Eleazara ndi Itamara.+