Salimo 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu inu, imbani nyimbo motsagana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda Yehova amene akukhala m’Ziyoni.+Fotokozani ntchito zake kwa mitundu ya anthu.+ Salimo 76:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malo ake opumulirako ali ku Salemu,+Malo ake okhalamo ali ku Ziyoni.+ Salimo 135:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova amene akukhala ku Yerusalemu,+Atamandidwe mu Ziyoni.+Tamandani Ya, anthu inu!+
11 Anthu inu, imbani nyimbo motsagana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda Yehova amene akukhala m’Ziyoni.+Fotokozani ntchito zake kwa mitundu ya anthu.+