Yoswa 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno atsogoleriwo anawauza kuti: “Akhale ndi moyo, ndipo akhale otola nkhuni ndi otungira madzi khamu lonse la Isiraeli,+ monga mmene tinawalonjezera.”+ Yoswa 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chotero pa tsikuli, Yoswa anawaika+ kukhala otola nkhuni ndi otungira madzi Aisiraeli,+ ndiponso kuti azitola nkhuni ndi kutunga madzi a paguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero. 1 Mbiri 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Oyamba kubwerera n’kukakhala ku cholowa chawo m’mizinda yawo anali Aisiraeli,+ ansembe,+ Alevi,+ ndi Anetini.+ Ezara 2:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Anetini+ onse pamodzi ndi ana a atumiki a Solomo analipo 392.+ Nehemiya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anetini+ anali kukhala ku Ofeli.+ Iwonso anakonza mpandawo mpaka kukafika ku Chipata cha Kumadzi,+ kum’mawa. Iwo anakonzanso nsanja yotundumukira kunja kwa mpanda.
21 Ndiyeno atsogoleriwo anawauza kuti: “Akhale ndi moyo, ndipo akhale otola nkhuni ndi otungira madzi khamu lonse la Isiraeli,+ monga mmene tinawalonjezera.”+
27 Chotero pa tsikuli, Yoswa anawaika+ kukhala otola nkhuni ndi otungira madzi Aisiraeli,+ ndiponso kuti azitola nkhuni ndi kutunga madzi a paguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.
2 Oyamba kubwerera n’kukakhala ku cholowa chawo m’mizinda yawo anali Aisiraeli,+ ansembe,+ Alevi,+ ndi Anetini.+
26 Anetini+ anali kukhala ku Ofeli.+ Iwonso anakonza mpandawo mpaka kukafika ku Chipata cha Kumadzi,+ kum’mawa. Iwo anakonzanso nsanja yotundumukira kunja kwa mpanda.