1 Mbiri 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Amenewa ndiwo anali oimba,+ atsogoleri a makolo a Alevi m’zipinda zodyera.+ Iwo sanali kupatsidwa ntchito zina+ chifukwa usana ndi usiku anali ndi udindo wogwira ntchito yawo.+ Ezara 2:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Oimba, ana a Asafu,+ 128.
33 Amenewa ndiwo anali oimba,+ atsogoleri a makolo a Alevi m’zipinda zodyera.+ Iwo sanali kupatsidwa ntchito zina+ chifukwa usana ndi usiku anali ndi udindo wogwira ntchito yawo.+