6 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, pamene asilikali anali kubwerera, Davide atakantha Mfilisiti uja, akazi anayamba kutuluka m’mizinda yonse ya Isiraeli akuimba nyimbo+ ndi kuvina. Iwo anali kupita kukachingamira mfumu Sauli mosangalala,+ akuimba maseche+ komanso choimbira cha zingwe zitatu.