Levitiko 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘M’mwezi wa 7,+ pa tsiku loyamba m’mweziwo, muzipuma pa ntchito zanu zonse. Limeneli ndi tsiku la chikumbutso, tsiku loliza lipenga,+ tsiku la msonkhano wopatulika.+ 1 Mafumu 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho anthu onse a mu Isiraeli anasonkhana kwa Mfumu Solomo pachikondwerero+ cha m’mwezi wa Etanimu, womwe ndi mwezi wa 7.+ Ezara 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pofika mwezi wa 7,+ ana a Isiraeli anali akukhala m’mizinda yawo. Ndiyeno anthuwo anayamba kusonkhana ku Yerusalemu+ monga munthu mmodzi.+
24 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘M’mwezi wa 7,+ pa tsiku loyamba m’mweziwo, muzipuma pa ntchito zanu zonse. Limeneli ndi tsiku la chikumbutso, tsiku loliza lipenga,+ tsiku la msonkhano wopatulika.+
2 Choncho anthu onse a mu Isiraeli anasonkhana kwa Mfumu Solomo pachikondwerero+ cha m’mwezi wa Etanimu, womwe ndi mwezi wa 7.+
3 Pofika mwezi wa 7,+ ana a Isiraeli anali akukhala m’mizinda yawo. Ndiyeno anthuwo anayamba kusonkhana ku Yerusalemu+ monga munthu mmodzi.+