Ekisodo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Isiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “N’chiyani ichi?” Chifukwa sanadziwe kuti chinali chiyani. Pamenepo Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+ Numeri 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Manawo+ anali ngati mapira,*+ ndipo maonekedwe ake anali ngati utomoni woonekera mkati ngati galasi.+ Yoswa 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mana analeka kugwa pa tsikuli, pamene ana a Isiraeli anadya zokolola za m’dzikomo. Kuyambira pamenepo, mana sanagwenso pakati pa ana a Isiraeli.+ Chotero, chaka chimenechi n’chimene iwo anayamba kudya zokolola za m’dziko la Kanani.+
15 Ana a Isiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “N’chiyani ichi?” Chifukwa sanadziwe kuti chinali chiyani. Pamenepo Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+
7 Manawo+ anali ngati mapira,*+ ndipo maonekedwe ake anali ngati utomoni woonekera mkati ngati galasi.+
12 Mana analeka kugwa pa tsikuli, pamene ana a Isiraeli anadya zokolola za m’dzikomo. Kuyambira pamenepo, mana sanagwenso pakati pa ana a Isiraeli.+ Chotero, chaka chimenechi n’chimene iwo anayamba kudya zokolola za m’dziko la Kanani.+