1 Samueli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakulanditsani m’manja mwa adani anu onse okuzungulirani, kuti mukhale popanda chokuopsani.+ 2 Mafumu 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova anali atalonjeza kuti sadzachotseratu dzina la Isiraeli padziko lapansi,+ choncho anawapulumutsa+ ndi dzanja la Yerobowamu mwana wa Yehoasi.
11 Pamenepo Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakulanditsani m’manja mwa adani anu onse okuzungulirani, kuti mukhale popanda chokuopsani.+
27 Yehova anali atalonjeza kuti sadzachotseratu dzina la Isiraeli padziko lapansi,+ choncho anawapulumutsa+ ndi dzanja la Yerobowamu mwana wa Yehoasi.