-
Nehemiya 8:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno Nehemiya+ amene ndiye Tirisata+ komanso Ezara+ wansembe, wokopera Malemba, ndi Alevi amene anali kupereka malangizo kwa anthu, anauza anthuwo kuti: “Lero ndi tsiku lopatulika kwa Yehova Mulungu wanu.+ Musakhale achisoni ndipo musalire.”+ Ananena zimenezi chifukwa anthu onse anali kulira pamene anali kumvetsera mawu a m’chilamulo.+
-