Ezara 2:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Pa chifukwa chimenechi, Tirisata*+ anawauza kuti sayenera kudya+ zinthu zopatulika koposa, kufikira patakhala wansembe wokhala ndi Urimu+ ndi Tumimu. Nehemiya 7:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Ndiye panali atsogoleri+ ena a nyumba za makolo+ amene anapereka mphatso zothandizira pa ntchito.+ Tirisata+ anapereka ndalama za dalakima* zagolide 1,000, mbale zikuluzikulu 50, ndi mikanjo ya ansembe 530 kumalo osungira chuma.+
63 Pa chifukwa chimenechi, Tirisata*+ anawauza kuti sayenera kudya+ zinthu zopatulika koposa, kufikira patakhala wansembe wokhala ndi Urimu+ ndi Tumimu.
70 Ndiye panali atsogoleri+ ena a nyumba za makolo+ amene anapereka mphatso zothandizira pa ntchito.+ Tirisata+ anapereka ndalama za dalakima* zagolide 1,000, mbale zikuluzikulu 50, ndi mikanjo ya ansembe 530 kumalo osungira chuma.+