2 Samueli 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni, malo okhala mumpanda wolimba kwambiri,+ umene ndi Mzinda wa Davide.+ 2 Samueli 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Davide anayamba kukhala m’malo okhala mumpanda wolimba kwambiri, ndipo anawatcha Mzinda wa Davide. Iye anayamba kumanga malo onsewo kuyambira ku Chimulu cha Dothi*+ mpaka mkati.
7 Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni, malo okhala mumpanda wolimba kwambiri,+ umene ndi Mzinda wa Davide.+
9 Davide anayamba kukhala m’malo okhala mumpanda wolimba kwambiri, ndipo anawatcha Mzinda wa Davide. Iye anayamba kumanga malo onsewo kuyambira ku Chimulu cha Dothi*+ mpaka mkati.