Numeri 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chakhumicho ndicho chizikhala chopereka chanu, monga cha tirigu wochokera pamalo popunthira,+ ndi cha vinyo wochuluka wochokera mopondera mphesa, kapena cha mafuta ochuluka ochokera m’chofinyira mafuta.
27 Chakhumicho ndicho chizikhala chopereka chanu, monga cha tirigu wochokera pamalo popunthira,+ ndi cha vinyo wochuluka wochokera mopondera mphesa, kapena cha mafuta ochuluka ochokera m’chofinyira mafuta.