Esitere 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mfumu inawalola kuchita zimenezi m’zigawo zonse za Mfumu Ahasiwero pa tsiku limodzi,+ tsiku la 13+ la mwezi wa 12 umene ndi mwezi wa Adara.*+
12 Mfumu inawalola kuchita zimenezi m’zigawo zonse za Mfumu Ahasiwero pa tsiku limodzi,+ tsiku la 13+ la mwezi wa 12 umene ndi mwezi wa Adara.*+