Numeri 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano Balamu anauza Balaki kuti: “Mundimangire pamalo ano maguwa ansembe+ okwanira 7. Mukatero mundikonzere ng’ombe zamphongo 7, ndi nkhosa zamphongo 7.”
23 Tsopano Balamu anauza Balaki kuti: “Mundimangire pamalo ano maguwa ansembe+ okwanira 7. Mukatero mundikonzere ng’ombe zamphongo 7, ndi nkhosa zamphongo 7.”