Salimo 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndani angazindikire yekha zinthu zimene walakwitsa?+Mundikhululukire machimo amene ndachita mosadziwa.+ Salimo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso mundiletse kuchita modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+Pamenepo ndidzakhala wopanda chifukwa,+Ndipo ndidzakhalabe wopanda milandu yambiri yophwanya malamulo. Miyambo 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Menya wonyoza+ kuti wosadziwa zinthu achenjere.+ Ndipo womvetsa zinthu uyenera kum’dzudzula kuti adziwe zinthu zowonjezereka.+
12 Ndani angazindikire yekha zinthu zimene walakwitsa?+Mundikhululukire machimo amene ndachita mosadziwa.+
13 Komanso mundiletse kuchita modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+Pamenepo ndidzakhala wopanda chifukwa,+Ndipo ndidzakhalabe wopanda milandu yambiri yophwanya malamulo.
25 Menya wonyoza+ kuti wosadziwa zinthu achenjere.+ Ndipo womvetsa zinthu uyenera kum’dzudzula kuti adziwe zinthu zowonjezereka.+