Salimo 35:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atandiona ndikuyenda motsimphina anasangalala ndipo anasonkhana pamodzi.+Anasonkhana pamodzi kuti alimbane nane.+Anandimenya pamene sindinali kuyembekezera.+Anandikhadzulakhadzula ndipo sanakhale chete.+
15 Atandiona ndikuyenda motsimphina anasangalala ndipo anasonkhana pamodzi.+Anasonkhana pamodzi kuti alimbane nane.+Anandimenya pamene sindinali kuyembekezera.+Anandikhadzulakhadzula ndipo sanakhale chete.+