Yobu 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndakhala chinthu choseketsa kwa anthu anzanga,+Ndakhala munthu woitana kwa Mulungu kuti amuyankhe.+Munthu wolungama ndi wosalakwa wakhala choseketsa.
4 Ine ndakhala chinthu choseketsa kwa anthu anzanga,+Ndakhala munthu woitana kwa Mulungu kuti amuyankhe.+Munthu wolungama ndi wosalakwa wakhala choseketsa.