Miyambo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kunyada kumafikitsa munthu ku chiwonongeko,+ ndipo mtima wodzikuza umachititsa munthu kupunthwa.+ Miyambo 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kudzikuza kwa munthu wochokera kufumbi kudzamutsitsa,+ koma wa mtima wodzichepetsa adzapeza ulemerero.+ Yakobo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe, kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu amapereka kumaposa khalidwe limeneli.+ N’chifukwa chake lemba limati: “Mulungu amatsutsa odzikweza,+ koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.”+ 1 Petulo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chimodzimodzinso inu anyamata. Muzigonjera+ amuna achikulire. Koma nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa,+ chifukwa Mulungu amatsutsa odzikweza, koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+
23 Kudzikuza kwa munthu wochokera kufumbi kudzamutsitsa,+ koma wa mtima wodzichepetsa adzapeza ulemerero.+
6 Komabe, kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu amapereka kumaposa khalidwe limeneli.+ N’chifukwa chake lemba limati: “Mulungu amatsutsa odzikweza,+ koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.”+
5 Chimodzimodzinso inu anyamata. Muzigonjera+ amuna achikulire. Koma nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa,+ chifukwa Mulungu amatsutsa odzikweza, koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+