2 Mafumu 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri+ n’kukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka m’mawa, anangoona kuti onse aja ndi mitembo yokhayokha.+ Danieli 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu wanga+ watumiza mngelo wake+ kudzatseka pakamwa pa mikango.+ Chotero mikangoyo sinandivulaze, chifukwa iye sanandipeze ndi mlandu uliwonse+ ndiponso sindinakulakwireni chilichonse inu mfumu.”+
35 Ndiyeno usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri+ n’kukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka m’mawa, anangoona kuti onse aja ndi mitembo yokhayokha.+
22 Mulungu wanga+ watumiza mngelo wake+ kudzatseka pakamwa pa mikango.+ Chotero mikangoyo sinandivulaze, chifukwa iye sanandipeze ndi mlandu uliwonse+ ndiponso sindinakulakwireni chilichonse inu mfumu.”+