Salimo 62:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ndithudi, moyo wanga ukuyembekezera Mulungu modekha.+Chipulumutso changa chidzachokera kwa iye.+ Maliro 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndi bwino kuti munthu ayembekezere+ chipulumutso cha Yehova+ moleza mtima.+