Salimo 35:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwo salankhula mawu amtendere,+Koma amakonzera chiwembu anthu ofatsa a padziko lapansi,Kuti awachitire zachinyengo.+ Miyambo 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 chifukwa mtima wawo umangokhalira kuganizira zolanda zinthu za ena, ndipo milomo yawo imangokhalira kunena zobweretsera ena mavuto.+
20 Iwo salankhula mawu amtendere,+Koma amakonzera chiwembu anthu ofatsa a padziko lapansi,Kuti awachitire zachinyengo.+
2 chifukwa mtima wawo umangokhalira kuganizira zolanda zinthu za ena, ndipo milomo yawo imangokhalira kunena zobweretsera ena mavuto.+