Salimo 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu Yehova, musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndaitana pa dzina lanu.+Anthu oipa achite manyazi.+Akhale chete m’Manda.+ Salimo 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kunyozeka.+Amene akundikonzera chiwembu muwabweze ndipo athedwe nzeru.+ Salimo 70:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+ Salimo 71:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu otsutsana nane achite manyazi, iwo awonongedwe.+Amene akufunafuna kundigwetsera tsoka adziphimbe ndi chitonzo ndiponso manyazi.+
17 Inu Yehova, musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndaitana pa dzina lanu.+Anthu oipa achite manyazi.+Akhale chete m’Manda.+
4 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kunyozeka.+Amene akundikonzera chiwembu muwabweze ndipo athedwe nzeru.+
2 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+
13 Anthu otsutsana nane achite manyazi, iwo awonongedwe.+Amene akufunafuna kundigwetsera tsoka adziphimbe ndi chitonzo ndiponso manyazi.+