Deuteronomo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti ndi mtundu winanso uti wamphamvu+ umene milungu yake ili pafupi nawo, monga mmene Yehova Mulungu wathu alili pafupi ndi ife, tikamaitanira pa iye+ nthawi zonse? Salimo 145:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova ali pafupi ndi onse oitanira pa iye.+Iye ali pafupi ndi onse amene amamuitana m’choonadi,+ Nahumu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo+ pa tsiku la nsautso.+ Amadziwa amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+
7 Pakuti ndi mtundu winanso uti wamphamvu+ umene milungu yake ili pafupi nawo, monga mmene Yehova Mulungu wathu alili pafupi ndi ife, tikamaitanira pa iye+ nthawi zonse?
7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo+ pa tsiku la nsautso.+ Amadziwa amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+