2 Mbiri 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ndidzasankha Yerusalemu+ kuti dzina langa likhale kumeneko, ndiponso ndidzasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’+ Salimo 48:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Mumzinda wa Mulungu wathu,+ m’phiri lake loyera.+ Yesaya 60:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ana a anthu okusautsa adzabwera kwa iwe atawerama.+ Onse amene anali kukuchitira chipongwe adzagwada pamapazi ako,+ ndipo adzakutcha mzinda wa Yehova, Ziyoni+ wa Woyera wa Isiraeli.
6 Koma ndidzasankha Yerusalemu+ kuti dzina langa likhale kumeneko, ndiponso ndidzasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’+
48 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Mumzinda wa Mulungu wathu,+ m’phiri lake loyera.+
14 “Ana a anthu okusautsa adzabwera kwa iwe atawerama.+ Onse amene anali kukuchitira chipongwe adzagwada pamapazi ako,+ ndipo adzakutcha mzinda wa Yehova, Ziyoni+ wa Woyera wa Isiraeli.