Salimo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga,+ nditayang’ana kumene kuli chipinda chamkati cha m’malo anu opatulika.+ Salimo 143:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+
2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga,+ nditayang’ana kumene kuli chipinda chamkati cha m’malo anu opatulika.+
7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+