Salimo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+ Salimo 56:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndimadalira Mulungu. Sindidzaopa.+Kodi munthu wochokera kufumbi angandichite chiyani?+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+ Aheberi 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Moti tikhale olimba mtima ndithu+ ndipo tinene kuti: “Yehova* ndiye mthandizi wanga. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+
27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
6 Moti tikhale olimba mtima ndithu+ ndipo tinene kuti: “Yehova* ndiye mthandizi wanga. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+