Salimo 59:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti, taonani! Iwo akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+Inu Yehova, anthu amphamvu akundiukira,+Ngakhale kuti ine sindinapanduke kapena kuchita tchimo lililonse.+ Salimo 71:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti adani anga anena za ine,+Ndipo anthu olondalonda moyo wanga, onse pamodzi achita upo,+
3 Pakuti, taonani! Iwo akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+Inu Yehova, anthu amphamvu akundiukira,+Ngakhale kuti ine sindinapanduke kapena kuchita tchimo lililonse.+