Yobu 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 N’chifukwa chiyani Mulungu amapereka kuwala kwa munthu amene ali ndi mavuto,Ndiponso moyo kwa opwetekedwa mtima?+ Yobu 33:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kum’bweza kuti asapite kudzenje,+Kuti aunikiridwe ndi kuwala kwa anthu amene ali moyo.+ Salimo 116:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzayenda+ pamaso pa Yehova m’dziko la anthu amoyo.+
20 N’chifukwa chiyani Mulungu amapereka kuwala kwa munthu amene ali ndi mavuto,Ndiponso moyo kwa opwetekedwa mtima?+