Salimo 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amadya ndi kukhuta chakudya chonona m’nyumba mwanu.+Ndipo mumawamwetsa mumtsinje wa zosangalatsa zanu zambiri.+ Salimo 63:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Moyo wanga wakhutira ndi gawo labwino kwambiri, wakhutira ndi zinthu zabwino kwambiri,+Ndipo milomo yanga ikukutamandani ndi mfuu yachisangalalo.+
8 Amadya ndi kukhuta chakudya chonona m’nyumba mwanu.+Ndipo mumawamwetsa mumtsinje wa zosangalatsa zanu zambiri.+
5 Moyo wanga wakhutira ndi gawo labwino kwambiri, wakhutira ndi zinthu zabwino kwambiri,+Ndipo milomo yanga ikukutamandani ndi mfuu yachisangalalo.+