Salimo 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pulumutsani anthu anu, ndipo dalitsani cholowa chanu.+Mukhale m’busa wawo ndipo muwanyamule mpaka kalekale.+ 2 Akorinto 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye Yesu Khristu, chikondi cha Mulungu, komanso mzimu woyera umene mukupindula nawo limodzi, zikhale nanu nonsenu.+ Aefeso 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamandike Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti watidalitsa+ ndi dalitso lililonse lauzimu m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu.
9 Pulumutsani anthu anu, ndipo dalitsani cholowa chanu.+Mukhale m’busa wawo ndipo muwanyamule mpaka kalekale.+
14 Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye Yesu Khristu, chikondi cha Mulungu, komanso mzimu woyera umene mukupindula nawo limodzi, zikhale nanu nonsenu.+
3 Atamandike Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti watidalitsa+ ndi dalitso lililonse lauzimu m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu.