Salimo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzawononga olankhula bodza.+Munthu wokhetsa magazi+ ndi wachinyengo,+ Yehova amaipidwa naye. Salimo 59:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa cha tchimo la pakamwa pawo, ndi mawu a pamilomo yawo.+Agwidwe chifukwa cha kunyada kwawo,+Chifukwa cha kutukwana ndi chinyengo zimene amachita mobwerezabwereza. Aroma 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ndipo m’kamwa mwawo mwadzaza mawu otukwana ndi opweteka.”+ 1 Petulo 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti “amene akufuna kusangalala ndi moyo ndi kuona masiku abwino,+ aletse lilime+ lake kuti lisalankhule zoipa ndi milomo yake kuti isalankhule chinyengo,+
12 Chifukwa cha tchimo la pakamwa pawo, ndi mawu a pamilomo yawo.+Agwidwe chifukwa cha kunyada kwawo,+Chifukwa cha kutukwana ndi chinyengo zimene amachita mobwerezabwereza.
10 Pakuti “amene akufuna kusangalala ndi moyo ndi kuona masiku abwino,+ aletse lilime+ lake kuti lisalankhule zoipa ndi milomo yake kuti isalankhule chinyengo,+