Yobu 38:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ikamyata m’malo amene imabisala,+Kapena ikabisala patchire kuti igwire nyama? Maliro 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kwa ine, iye ali ngati chimbalangondo chimene chandibisalira,+ ndiponso ngati mkango umene wakhala pamalo obisika.+
10 Kwa ine, iye ali ngati chimbalangondo chimene chandibisalira,+ ndiponso ngati mkango umene wakhala pamalo obisika.+