Salimo 119:171 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 171 Milomo yanga itulutse mawu okutamandani,+Pakuti mwandiphunzitsa malamulo anu.+ Miyambo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 kuti azitha kumvetsa mwambi ndi mawu ozunguza mutu,+ mawu a anthu anzeru+ ndi mikuluwiko yawo.+ Miyambo 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mawu a m’kamwa mwa munthu ndiwo madzi akuya.+ Chitsime cha nzeru chili ngati mtsinje wosefukira.+ Ezekieli 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, phera nyumba ya Isiraeli mwambi+ ndipo uwauze mawu ophiphiritsa.+