Salimo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+
7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+