Salimo 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti waumphawi sadzaiwalidwa nthawi zonse,+Ndiponso chiyembekezo cha ofatsa sichidzatha konse.+ Salimo 147:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova amathandiza anthu ofatsa,+Koma anthu oipa amawagwetsera pansi.+