Salimo 89:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Inu Yehova, kodi mudzadzibisa kufikira liti? Ku nthawi zonse?+Kodi mkwiyo wanu udzakhalabe ukuyaka ngati moto?+ Yesaya 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Taonani! Dzina la Yehova likubwera kuchokera kutali. Likubwera ndi mkwiyo woyaka+ ndiponso mitambo yolemera. Pamilomo yake padzaza mawu odzudzula ndipo lilime lake lili ngati moto wowononga.+ Zefaniya 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Siliva kapena golide wawo sadzawapulumutsa pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+ Moto wa mkwiyo wake udzanyeketsa dziko lonse lapansi,+ chifukwa iye adzafafaniza anthu onse okhala padziko lapansi.”+ 2 Atesalonika 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango+ kwa anthu osadziwa Mulungu+ ndi kwa anthu osamvera uthenga wabwino+ wonena za Ambuye wathu Yesu.+
46 Inu Yehova, kodi mudzadzibisa kufikira liti? Ku nthawi zonse?+Kodi mkwiyo wanu udzakhalabe ukuyaka ngati moto?+
27 Taonani! Dzina la Yehova likubwera kuchokera kutali. Likubwera ndi mkwiyo woyaka+ ndiponso mitambo yolemera. Pamilomo yake padzaza mawu odzudzula ndipo lilime lake lili ngati moto wowononga.+
18 Siliva kapena golide wawo sadzawapulumutsa pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+ Moto wa mkwiyo wake udzanyeketsa dziko lonse lapansi,+ chifukwa iye adzafafaniza anthu onse okhala padziko lapansi.”+
8 Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango+ kwa anthu osadziwa Mulungu+ ndi kwa anthu osamvera uthenga wabwino+ wonena za Ambuye wathu Yesu.+