Salimo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pali ambiri amene akunena kuti: “Ndani adzationetsa zinthu zabwino?”Inu Yehova, tiunikeni ndi kuwala kwa nkhope yanu.+
6 Pali ambiri amene akunena kuti: “Ndani adzationetsa zinthu zabwino?”Inu Yehova, tiunikeni ndi kuwala kwa nkhope yanu.+