Yesaya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova+ atakhala pampando wachifumu+ wolemekezeka umene unali pamalo okwezeka, ndipo zovala zake zinadzaza m’kachisi.+ Mika 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tamverani anthu nonsenu. Mvetsera mwatcheru iwe dziko lapansi ndi anthu onse okhala mwa iwe.+ Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa akhale mboni yokutsutsani pa zimene mukuchita.+ Yehova akutsutseni ali m’kachisi wake woyera.+ Habakuku 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+ Inu anthu onse a padziko lapansi, khalani chete pamaso pake!’”+ Chivumbulutso 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’chifukwa chake ali pamaso+ pa mpando wachifumu wa Mulungu. Iwo akumuchitira utumiki wopatulika+ usana ndi usiku m’kachisi wake, ndipo wokhala pampando wachifumuyo+ adzatambasulira hema+ wake pamwamba pawo kuti awateteze.
6 M’chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova+ atakhala pampando wachifumu+ wolemekezeka umene unali pamalo okwezeka, ndipo zovala zake zinadzaza m’kachisi.+
2 “Tamverani anthu nonsenu. Mvetsera mwatcheru iwe dziko lapansi ndi anthu onse okhala mwa iwe.+ Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa akhale mboni yokutsutsani pa zimene mukuchita.+ Yehova akutsutseni ali m’kachisi wake woyera.+
20 Koma Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+ Inu anthu onse a padziko lapansi, khalani chete pamaso pake!’”+
15 N’chifukwa chake ali pamaso+ pa mpando wachifumu wa Mulungu. Iwo akumuchitira utumiki wopatulika+ usana ndi usiku m’kachisi wake, ndipo wokhala pampando wachifumuyo+ adzatambasulira hema+ wake pamwamba pawo kuti awateteze.