Salimo 53:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi palibe aliyense wozindikira mwa anthu ochita zopweteka anzawowa,+Amene akudya anthu anga ngati chakudya?+Iwo sanaitane pa Yehova.+ Mika 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndinapitiriza kunena kuti: “Tamverani inu atsogoleri a mbadwa za Yakobo ndi inu olamulira a nyumba ya Isiraeli.+ Kodi si inu oyenera kudziwa chilungamo?+
4 Kodi palibe aliyense wozindikira mwa anthu ochita zopweteka anzawowa,+Amene akudya anthu anga ngati chakudya?+Iwo sanaitane pa Yehova.+
3 Ine ndinapitiriza kunena kuti: “Tamverani inu atsogoleri a mbadwa za Yakobo ndi inu olamulira a nyumba ya Isiraeli.+ Kodi si inu oyenera kudziwa chilungamo?+