2 Mafumu 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga,+Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+ Salimo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 N’chifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita chipolowe,+Ndiponso n’chifukwa chiyani mitundu ya anthu ikung’ung’udza za chinthu chopanda pake?+ Salimo 74:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu amene akukuchitirani zoipa afuula mosangalala kuti apambana m’malo anu olambiriramo.+Aikamo mbendera zawo monga zizindikiro.+ Machitidwe 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinu amene mwa mzimu woyera, munanena kudzera pakamwa pa kholo lathu Davide,+ mtumiki wanu kuti, ‘N’chifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita chipolowe, ndiponso n’chifukwa chiyani mitundu ya anthu ikusinkhasinkha zinthu zopanda pake?+
28 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga,+Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+
2 N’chifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita chipolowe,+Ndiponso n’chifukwa chiyani mitundu ya anthu ikung’ung’udza za chinthu chopanda pake?+
4 Anthu amene akukuchitirani zoipa afuula mosangalala kuti apambana m’malo anu olambiriramo.+Aikamo mbendera zawo monga zizindikiro.+
25 Ndinu amene mwa mzimu woyera, munanena kudzera pakamwa pa kholo lathu Davide,+ mtumiki wanu kuti, ‘N’chifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita chipolowe, ndiponso n’chifukwa chiyani mitundu ya anthu ikusinkhasinkha zinthu zopanda pake?+