Salimo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wabwino ndi wolungama.+N’chifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende m’njira yoyenera.+ Salimo 145:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova amakomera mtima aliyense,+Ndipo ntchito zake zonse amazichitira chifundo.+ Luka 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yesu anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino? Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+
8 Yehova ndi wabwino ndi wolungama.+N’chifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende m’njira yoyenera.+
19 Yesu anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino? Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+