6 Ndiyeno iye anatumiza uthenga kwa Baraki+ mwana wa Abinowamu, yemwe anali ku Kedesi-nafitali,+ womuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli walamula kuti, ‘Tenga amuna 10,000 pakati pa ana a Nafitali+ ndi ana a Zebuloni+ ndipo mukasonkhane paphiri la Tabori.+