Salimo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu odziwa dzina lanu adzakukhulupirirani,+Pakuti simudzasiya ndithu anthu okufunafunani, inu Yehova.+ Miyambo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.+ Yeremiya 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Choncho ine ndiwaphunzitsa. Pa nthawi ino yokha ndiwaonetsa dzanja langa ndi mphamvu zanga,+ ndipo adziwa kuti dzina langa ndine Yehova.”+ Yohane 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+
10 Anthu odziwa dzina lanu adzakukhulupirirani,+Pakuti simudzasiya ndithu anthu okufunafunani, inu Yehova.+
21 “Choncho ine ndiwaphunzitsa. Pa nthawi ino yokha ndiwaonetsa dzanja langa ndi mphamvu zanga,+ ndipo adziwa kuti dzina langa ndine Yehova.”+
3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+