Ekisodo 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho anthuwo anaimabe patali pomwepo, koma Mose anayandikira mtambo wakuda uja kumene kunali Mulungu woona.+ 1 Mafumu 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawi imeneyo Solomo anati: “Yehova anati adzakhala mu mdima wandiweyani.+ Salimo 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako anapanga mdima kukhala malo ake obisalamo,+Panali madzi akuda ndi mtambo wakuda,Zimene zinamuzungulira ngati msasa wake.+
21 Choncho anthuwo anaimabe patali pomwepo, koma Mose anayandikira mtambo wakuda uja kumene kunali Mulungu woona.+
11 Kenako anapanga mdima kukhala malo ake obisalamo,+Panali madzi akuda ndi mtambo wakuda,Zimene zinamuzungulira ngati msasa wake.+