Salimo 95:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tiyeni tionekere pamaso pake ndi chiyamiko.+Tiyeni tiimbe nyimbo zomutamanda ndi kumufuulira mosangalala chifukwa wapambana.+
2 Tiyeni tionekere pamaso pake ndi chiyamiko.+Tiyeni tiimbe nyimbo zomutamanda ndi kumufuulira mosangalala chifukwa wapambana.+