Salimo 96:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imbirani Yehova, tamandani dzina lake.+Tsiku ndi tsiku lengezani uthenga wabwino wa chipulumutso chake.+ Salimo 145:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 145 Ndidzakukwezani, inu Mfumu ndi Mulungu wanga,+Ndipo ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+
2 Imbirani Yehova, tamandani dzina lake.+Tsiku ndi tsiku lengezani uthenga wabwino wa chipulumutso chake.+
145 Ndidzakukwezani, inu Mfumu ndi Mulungu wanga,+Ndipo ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+