Salimo 51:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chitirani Ziyoni zabwino mwa kukoma mtima kwanu.+Ndipo mangani mpanda wa Yerusalemu.+ Salimo 147:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova akumanga Yerusalemu.+Anthu okhala mu Isiraeli amene anabalalika akuwasonkhanitsanso pamodzi.+ Yeremiya 33:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndibwezeretsa anthu a mu Yuda ndi a mu Isiraeli amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,+ ndipo ndiwalimbitsa kuti akhale ngati mmene analili poyamba.+
2 Yehova akumanga Yerusalemu.+Anthu okhala mu Isiraeli amene anabalalika akuwasonkhanitsanso pamodzi.+
7 Ndibwezeretsa anthu a mu Yuda ndi a mu Isiraeli amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,+ ndipo ndiwalimbitsa kuti akhale ngati mmene analili poyamba.+